Psalms 78:39 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ankakumbukira kuti iwo anali anthu chabe, ngati mphepo yopita imene siibwereranso.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anakumbukira kuti iwo ndiwo anthu; mphepo yopita yosabweranso.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anakumbukira kuti iwo anali anthu chabe, mphepo yopita imene sibwereranso.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anakumbukira kuti iwo ndiwo anthu; Mphepo yopita yosabweranso.