Psalms 78:44 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Paja Mulungu adasandutsa madzi a mitsinje yao kuti akhale magazi, kotero kuti Aejipito sadathe kumwa madziwo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nasanduliza nyanja yao mwazi, ndi mitsinje yao, kuti sangakhoze kumwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anasandutsa mitsinje yawo kukhala magazi; Iwo sanathe kumwa madzi ochokera mʼmitsinje yawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nasanduliza nyanja yao mwazi, Ndi mitsinje yao, kuti sangakhoze kumwa.