Psalms 78:46 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adalola kuti kapuchi adye mbeu zao ndiponso kuti dzombe lidye zonse za m'minda mwao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anapatsa mphuchi dzinthu dzao, ndi dzombe ntchito yao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anapereka mbewu zawo kwa ziwala, zokolola zawo kwa dzombe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anapatsa mphuci dzinthu dzao, Ndi dzombe nchito yao.