Psalms 78:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adapereka mau odzichitira umboni kwa Yakobe, adakhazikitsa malamulo ake mu Israele. Adalamula makolo athu kuti aziŵaphunzitsa ana ao malamulowo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anakhazika mboni mwa Yakobo, naika chilamulo mwa Israele, ndizo analamulira atate athu, akazidziwitse ana ao;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anapereka mawu wodzichitira umboni kwa Yakobo ndi kukhazikitsa lamulo mu Israeli, zimene analamulira makolo athu kuphunzitsa ana awo,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anakhazika mboni mwa Yakobo, Naika cilamulo mwa Israyeli, Ndizo analamulira atate athu, Akazidziwitse ana ao;