Psalms 78:51 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adapha ana achisamba onse a Aejipito, ana oyamba a mphamvu zao, m'zithando za zidzukulu za Hamu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anapha ana oyamba onse a mu Ejipito, ndiwo oyamba a mphamvu yao m'mahema a Hamu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anakantha ana oyamba kubadwa a Igupto, zipatso zoyamba kucha za mphamvu zawo mʼmatenti a Hamu
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anapha ana oyamba onse a mu Aigupto, Ndiwo oyamba a mphamvu yao m'mahema a Hamu: