Psalms 78:52 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Mulungu adaŵatulutsa anthu ake ngati nkhosa, naŵatsogolera m'chipululu ngati zoŵeta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma anatulutsa anthu ake ngati nkhosa, nawatsogoza ngati gulu la zoweta m'chipululu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Iye anatulutsa anthu ake ngati ziweto; anawatsogolera ngati nkhosa kudutsa mʼchipululu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma anaturutsa anthu ace ngati nkhosa, Nawatsogoza ngati gulu la zoweta m'cipululu.