Psalms 78:55 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adapirikitsa mitundu ina ya anthu, kuŵachotsa m'njira. Adagaŵagaŵa dziko la anthuwo kuti likhale la anthu ake, adakhazikitsa mafuko a Israele m'midzi ya anthuwo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anapirikitsa amitundu pamaso pao, nawagawira cholowa chao, ndi muyeso, nakhalitsa mafuko a Israele m'mahema mwao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anathamangitsa mitundu ya anthu patsogolo pawo ndipo anapereka mayiko awo kwa Aisraeli kuti akhale awo; Iye anakhazikitsa mafuko a Israeli mʼnyumba zawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anapitikitsa amitundu pamaso pao, Nawagawira colowa cao, ndi muyeso, Nakhalitsa mafuko a Israyeli m'mahema mwao.