Psalms 78:57 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
koma iwo adakhala okanika ndi osakhulupirika monga makolo ao. Adapotoka ngati uta wosakhulupirika.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
koma anabwerera m'mbuyo, nachita zosakhulupirika monga makolo ao, anapatuka ngati uta wolenda.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anakhala okanika ndi osakhulupirika monga makolo awo, anapotoka monga uta wosakhulupirika.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma anabwerera m'mbuyo, nacita zosakhulupirika monga makolo ao: Anapatuka ngati uta wolenda,