Psalms 78:62 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chifukwa adakwiyira anthu ake, adalola kuti anthu akewo aphedwe pa nkhondo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Naperekanso anthu ake kwa lupanga; nakwiya nacho cholandira chake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anapereka anthu ake ku lupanga; anakwiya kwambiri ndi cholowa chake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Naperekanso anthu ace kwa lupanga; Nakwiya naco colandira cace.