Psalms 78:65 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pomaliza Ambuye adachita ngati kudzuka kutulo, ngati munthu wamphamvu wofuula chifukwa choledzera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo Ambuye anauka ngati wam'tulo; ngati chiphona chakuchita nthungululu ndi vinyo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka Ambuye anakhala ngati akudzuka kutulo, ngati munthu wamphamvu wofuwula chifukwa cha vinyo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo Ambuye anauka ngati wam'tulo; Ngati ciphona cakucita nthungululu ndi vinyo.