Psalms 78:69 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adamanga malo ake opatulika ngati malo ake akumwamba, okhazikika ngati dziko lapansi mpaka muyaya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anamanga malo oyera ake ngati kaphiri, monga dziko lapansi limene analikhazikitsa kosatha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anamanga malo ake opatulika ngati zitunda, dziko limene analikhazikitsa kwamuyaya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anamanga malo oyera ace ngati kaphiri, Monga dziko lapansi limene analikhazikitsa kosatha.