Psalms 78:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anawo aike chikhulupiriro chao pa Mulungu, ndipo asaiŵale ntchito za Mulungu, koma asunge malamulo ake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi kuti chiyembekezo chao chikhale kwa Mulungu, osaiwala zochita Mulungu, koma kusunga malamulo ake ndiko.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho iwo adzakhulupirira Mulungu ndipo sadzayiwala ntchito zake koma adzasunga malamulo ake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi kuti ciyembekezo cao cikhale kwa Mulungu, Osaiwala zocita Mulungu, Koma kusunga malamulo ace ndiko.