Psalms 78:71 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adamtenga kumene ankaŵeta nkhosa zimene zinali ndi ana, kuti adzakhale mbusa wa Yakobe, fuko lake, wa Israele, choloŵa chake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anamtenga kuja anatsata zoyamwitsa, awete Yakobo, anthu ake, ndi Israele, cholandira chake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
kuchokera koyangʼanira nkhosa anamubweretsa kuti akhale mʼbusa wa anthu ake, Yakobo, wa Israeli cholowa chake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anamtenga kuja anatsata zoyamwitsa, Awete Yakobo, anthu ace, ndi Israyeli, colandira cace.