Psalms 78:72 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Davide adaŵasamala ndi mtima wolungama, naŵatsogolera ndi dzanja lake mwaluso.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Potero anawaweta monga mwa mtima wake wangwiro; nawatsogolera ndi luso la manja ake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo Davide anawaweta ndi mtima wolungama; ndi manja aluso anawatsogolera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Potero anawaweta monga mwa mtima wace wangwiro; Nawatsogolera ndi luso la manja ace.