Psalms 79:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mumve kubuula kwa anthu am'ndende, muŵasunge ndi mphamvu zanu zazikulu anthu oyenera kuphedwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kubuula kwa wandende kufike kuli Inu; monga mwa mphamvu yanu yaikulu lolani ana a imfa atsale.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kubuwula kwa anthu a mʼndende kufike pamaso panu; ndi mphamvu ya dzanja lanu muwasunge amene aweruzidwa kuti aphedwe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kubuula kwa wandende kufike kuli Inu; Monga mwa mphamvu yanu yaikuru lolani ana a imfa atsale;