Psalms 79:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ataya mitembo ya atumiki anu kwa mbalame zamumlengalenga, kuti ikhale chakudya chake, ataya matupi a anthu anu oyera mtima kwa zilombo zakuthengo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anapereka mitembo ya atumiki anu ikhale chakudya cha mbalame za mlengalenga, nyama ya okondedwa anu anaipereka kwa zilombo za m'dziko.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo anapereka mitembo ya atumiki anu kwa mbalame zamlengalenga ngati chakudya, matupi a oyera mtima anu kwa zirombo za dziko lapansi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anapereka mitembo ya atumiki anu ikhale cakudya ca mbalame za mlengalenga, Nyama ya okondedwa anu anaipereka kwa zirombo za m'dziko.