Psalms 79:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Akhetsa magazi ao ngati madzi, ponse pozungulira Yerusalemu, ndipo palibe woti nkuika maliro ao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anakhetsa mwazi wao ngati madzi pozungulira Yerusalemu; ndipo panalibe wakuwaika.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Akhetsa magazi monga madzi kuzungulira Yerusalemu yense, ndipo palibe wina woti ayike mʼmanda anthu akufa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anakhetsa mwazi wao ngati madzi pozungulira Yerusalemu; Ndipo panalibe wakuwaika.