Psalms 79:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ife tasanduka chinthu chonyozeka kwa anzathu, anthu a mitundu ina amatinyodola ndi kutiseka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Takhala chotonza cha anansi athu, ndi choseketsa ndi cholalatitsa iwo akutizinga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ife ndife chinthu chonyozeka kwa anansi athu, choseketsa ndi cholalatiridwa kwa iwo amene atizungulira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Takhala cotonza ca anansi athu, Ndi coseketsa ndi colalatitsa iwo akutizinga,