Psalms 79:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mpaka liti, Inu Chauta? Kodi mudzakhalabe wokwiya mpaka muyaya? Kodi nsanje yanu idzayakabe ngati moto?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yehova, mudzakwiya nthawi zonse kufikira liti? Nidzatentha nsanje yanu ngati moto?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mpaka liti Inu Yehova? Kodi mudzakwiya mpaka muyaya? Kodi mpaka liti nsanje yanu idzayaka ngati moto?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yehova, mudzakwiya nthawi zonse kufikira liti? Nidzatentha nsanje yanu ngati moto?