Psalms 79:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Gwetsani ukali wanu pa mitundu ya anthu osakudziŵani, ndiponso pa maufumu osatama dzina lanu mopemba.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Thirirani mkwiyo wanu pa akunja osadziwa Inu, ndi pa maufumu osaitana pa dzina lanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Khuthulirani ukali wanu pa anthu a mitundu ina amene sakudziwani Inu, pa maufumu amene sayitana pa dzina lanu;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Thirirani mkwiyo wanu pa akunja osadziwa Inu, Ndi pa maufumu osaitana pa dzina lanu.