Psalms 79:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pakuti ameza anthu a Yakobe, ndipo dziko lao alisandutsa bwinja.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti anathera Yakobo, napasula pokhalira iye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
pakuti iwo ameza Yakobo ndi kuwononga dziko lawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti anathera Yakobo, Napasula pokhalira iye.