Psalms 79:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Musatilange ife chifukwa cha machimo a makolo athu. Mutichitire chifundo msanga, chifukwa tatsitsidwa kwambiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Musakumbukire motitsutsa mphulupulu za makolo athu; nsoni zokoma zanu zitipeze msanga, pakuti tafooka kwambiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Musatilange chifukwa cha machimo a makolo athu chifundo chanu chibwere msanga kukumana nafe, pakuti tili ndi chosowa chachikulu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Musakumbukile moritsutsa mphulupulu za makolo athu; Nsoni zokoma zanu zitikumike msanga: Pakuti tafoka kwambiri.