Psalms 8:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nawonso ana ndi makanda omwe amauimbira. Mwamanga linga chifukwa cha adani anu, kuti mugonjetse onse okuukirani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
M'kamwa mwa makanda ndi oyamwa munakhazikitsa mphamvu, chifukwa cha otsutsana ndi Inu, kuti muwaletse mdani ndi wobwezera chilango.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kuchokera mʼkamwa mwa ana ndi makanda, Inu mwakhazikitsa mphamvu chifukwa cha adani anu, kukhazikitsa bata adani ndi anthu obwezera zoyipa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
M'kamwa mwa makanda ndi oyamwamunakhazikitsamphamvu, Cifukwa ca otsutsana ndi Inu, Kuti muwaletse mdani ndi wobwezera cilango.