Psalms 8:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndikamayang'ana ku thambo lanu limene mudapanga ndi manja anu, ndikamaona mwezi ndi nyenyezi zimene mudazikhazika kumeneko,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuona ine thambo la kumwamba lanu, ntchito ya zala zanu, mwezi ndi nyenyezi, zimene munazikhazika,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene ndilingalira za mayiko anu akumwamba, ntchito ya zala zanu, mwezi ndi nyenyezi, zimene mwaziyika pa malo ake,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuona ine thambo la kumwamba lanu, nchito ya zala zanu, Mwezi ndi nyenyezi, zimene munazikhazika,