Psalms 8:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ndimadzifunsa kuti, “Kodi munthu nchiyani kuti muzimkumbukira, mwana wa munthu nchiyani kuti muzimsamalira?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
munthu ndani kuti mumkumbukira? Ndi mwana wa munthu kuti mucheza naye?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
munthu ndani kuti Inu mumamukumbukira, ndi mwana wa munthu kuti inu mumacheza naye?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Munthu ndani kuti mumkumbukila? Ndi mwana wa munthu kuti muceza naye?