Psalms 8:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mudampatsa ulamuliro pa ntchito za manja anu. Mudamgonjetsera zolengedwa zonse,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Munamchititsa ufumu pa ntchito za manja anu; mudagonjetsa zonse pansi pa mapazi ake;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu munamuyika wolamulira ntchito ya manja anu; munayika zinthu zonse pansi pa mapazi ake;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Munamcititsa ufumu pa nchito za manja anu; Mudagonjetsa zonse pansi pa mapazi ace;