Psalms 80:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mapiri adaphimbidwa ndi mthunzi wake, mikungudza yaikulu yomwe idaphimbidwa ndi nthambi zake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mthunzi wake unaphimba mapiri, ndi nthambi zake zikunga mikungudza ya Mulungu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mapiri anaphimbidwa ndi mthunzi wake, mikungudza yamphamvu ndi nthambi zake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mthunzi wace unaphimba mapiri, Ndi nthambi zace zikunga mikungudza ya Mulungu.