Psalms 80:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nthambizo zidafika mpaka ku nyanja yaikulu yakuzambwe, ndipo mphukira zake mpaka ku mtsinje waukulu wakuvuma.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Unatambalitsa mphanda zake mpaka kunyanja, ndi mitsitsi yake kufikira ku Mtsinje.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Unatambalitsa nthambi zake mpaka ku nyanja, mphukira zake mpaka ku mtsinje.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Unatambalitsa mphanda zace mpaka kunyanja, Ndi mitsitsi yace kufikira ku Mtsinje.