Psalms 80:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nanga chifukwa chiyani mwagumula mpanda wake, kuti opita m'njira azithyola nawo zipatso zake?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Munapasuliranji maphambo ake, kotero kuti onse akupita m'njira atcherako?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chifukwa chiyani mwagwetsa makoma ake kuti onse amene akudutsa athyole mphesa zake?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Munapasuliranii maphambo ace, Kotero kuti onse akupita m'njira acherako?