Psalms 80:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adani athu autentha, augwetsa pansi. Ayang'aneni iwowo mokwiya ndi kuŵaononga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Unapserera ndi moto, unadulidwa; aonongeka pa kudzudzula kwa nkhope yanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mpesa wanu wadulidwa ndi kutenthedwa ndi moto; pakudzudzula kwanu anthu anu awonongeka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Unapserera ndi moto, unadulidwa; Aonongeka pa kudzudzula kwa nkhope yanu.