Psalms 80:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma ndi dzanja lanu muteteze anthu amene mudaŵasankha, anthu amene Inu nomwe mwaŵalimbikitsa kuti akutumikireni.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Dzanja lanu likhale pa munthu wa pa dzanja lamanja lanu; pa mwana wa munthu amene munadzilimbikitsira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Dzanja lanu likhale pa munthu amene ali ku dzanja lanu lamanja, mwana wa munthu amene mwalera nokha.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Dzanja lanu likhale pa munthu wa pa dzanja lamanja lanu; Pa mwana wa munthu amene munadzilimbikitsira.