Psalms 80:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu Chauta, Mulungu Wamphamvuzonse, mudzakwiyira mapemphero a anthu anu mpaka liti?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yehova, Mulungu wa makamu, mudzakwiyira pemphero la anthu anu kufikira liti?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu Mulungu Wamphamvuzonse, mpaka liti mkwiyo wanu udzanyeka kutsutsana ndi mapemphero a anthu anu?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yehova, Mulungu wa makamu, Mudzakwiyira pemphero la anthu anu kufikira liti?