Psalms 80:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mwaŵadyetsa chisoni ngati chakudya, mwaŵapatsa misozi ngati chakumwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Munawadyetsa mkate wa misozi, ndipo munawamwetsa misozi yambiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mwawadyetsa buledi wa misozi; mwachitisa iwo kumwa misozi yodzaza mbale.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Munawadyetsa mkate wa misozi, Ndipo munawamwetsa misozi yambiri.