Psalms 80:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mwaŵasandutsa chinthu chonyozeka kwa anzathu a mitundu ina, ndipo adani athu akakhala pamodzi, amangotiseka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mutiika kuti atilimbirane anzathu; ndipo adani athu atiseka mwa iwo okha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mwachititsa kuti tikhale gwero la mikangano pakati pa anansi athu, ndipo adani athu akutinyoza.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mutiika kuti atilimbirane anzathu; Ndipo adani athu atiseka mwa iwo okha,