Psalms 80:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mudatulutsa mpesa wanu Israele m'dziko la Ejipito. Mudapirikitsa mitundu ina ya anthu kuti muubzale mpesawo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mudatenga mpesa kuchokera ku Ejipito, munapirikitsa amitundu ndi kuuoka uwu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Munatulutsa mpesa kuchoka ku Igupto; munathamangitsa anthu a mitundu ina ndi kuwudzala mpesawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mudatenga mpesa kucokera ku Aigupto: Munapitikitsa amitundu ndi kuuoka uwu.