Psalms 81:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kwezani mau kuimbira Mulungu amene ali mphamvu zathu. Fuulani ndi chimwemwe kwa Mulungu wa Yakobe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kwa Mkulu wa Nyimbo, pa Gititi. Salimo la Asafu. Imbitsirani Mulungu ndiye mphamvu yathu; fuulirani kwa Mulungu wa Yakobo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kwa mtsogoleri wa mayimbidwe. Potsata mayimbidwe a gititi. Salimo la Asafu. Imbani mwachimwemwe kwa Mulungu mphamvu yathu; Fuwulani mokweza kwa Mulungu wa Yakobo!
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yimbitsirani Mulungu ndiye mphamvu yathu; Pfuulirani kwa Mulungu wa Yakobo.