Psalms 81:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Choncho ndidaŵasiya ndi mitima yao yosamverayo, kuti atsate zimene ankafuna.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Potero ndinawaperekera kuuma mtima kwao, ayende monga mwa uphungu waowao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kotero ndinawasiya ndi mitima yawo yosamverayo kuti atsate zimene ankafuna.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Potero ndinawaperekera kuuma mtima kwao, Ayende monga mwa uphungu wao wao.