Psalms 81:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Anthu amene amadana ndi Chauta, akadakhwinyata pamaso pake, ndipo tsoka lao likadakhala mpaka muyaya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Akumuda Yehova akadamgonjera mungakhale monyenga, koma nyengo yao ikadakhala yosatha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo amene amadana ndi Yehova akanakhwinyata pamaso pake, ndipo chilango chawo chinakakhala mpaka kalekale.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Akumuda Yehova akadamgonjera mungakhale monyenga: Koma nyengo yao ikadakhala yosatha,