Psalms 81:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndikadakudyetsani ndi ufa wosalala watirigu, ndipo ndikadakukhutitsani ndi uchi wam'thanthwe.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Akadawadyetsa naye tirigu wokometsetsa, ndikadakukhutitsanso ndi uchi wa m'thanthwe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma inu mukanadyetsedwa tirigu wabwino kwambiri; ndikanakukhutitsani ndi uchi wochokera pa thanthwe.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Akadawadyetsa naye tirigu wakometsetsa: Ndikadakukhutitsanso ndi uci wa m'thanthwe.