Psalms 81:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Imbani lipenga mwezi ukaoneka chatsopano, ukaoneka kwathunthu, pa tsiku lathu lachikondwerero.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ombani lipenga, pokhala mwezi, utakula mwezi, tsiku la phwando lathu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Imbani lipenga la nyanga ya nkhosa yayimuna pa mwezi watsopano, ndi pamene mwezi waoneka wonse, pa tsiku la phwando;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ombani lipenga, pokhala mwezi, Utakula mwezi, tsiku la phwando lathu.