Psalms 82:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Akuti, “Mudzakhalabe mukuweruza mopanda chilungamo mpaka liti? Bwanji mukupitirizabe kumakondera anthu oipa?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mudzaweruza mosalunjika kufikira liti, ndi kusamalira nkhope ya oipa?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Mudzateteza osalungama mpaka liti, ndi kukondera anthu oyipa?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mudzaweruza mosalunjika kufikira liti, Ndi kusamalira nkhope ya oipa?