Psalms 82:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iwo sadziŵa kanthu ndiponso alibe nzeru, amangoyenda m'chimbulimbuli. Maziko onse a dziko lapansi agwedezeka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Sadziwa, ndipo sazindikira; amayendayenda mumdima; maziko onse a dziko lapansi agwedezeka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Iwo sadziwa kanthu, sazindikira kalikonse. Amayendayenda mu mdima; maziko onse a dziko lapansi agwedezeka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Sadziwa, ndipo sazindikira; Amayendayenda mumdima; Maziko onse a dziko lapansi agwedezeka.