Psalms 82:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Komabe mudzafa ngati anthu onse, ndipo mudzagwa ngati kalonga wina aliyense.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Komatu mudzafa monga anthu, ndipo mudzagwa monga wina wa akulu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma mudzafa ngati anthu wamba; mudzagwa ngati wolamula wina aliyense.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Komatu mudzafa monga anthu, Ndipo mudzagwa monga wina wa akulu.