Psalms 82:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Dzambatukani, Inu Mulungu, weruzani dziko lapansi, popeza kuti mitundu yonse ya anthu ndi yanu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ukani, Mulungu, weruzani dziko lapansi; pakuti Inu mudzalandira amitundu onse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Dzukani Inu Mulungu, weruzani dziko lapansi, pakuti mayiko onse ndi cholowa chanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ukani, Mulungu, weruzani dziko lapansi; Pakuti Inu mudzalandira amitundu onse.