Psalms 83:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Akalonga ao muŵachite zomwe mudachita Orebu ndi Zeebu, ndipo ana a mafumu ao onse, muŵachite zomwe mudachita Zeba ndi Zalimuna,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Muwaike akulu ao ngati Orebu ndi Zeebu; mafumu ao ngati Zeba ndi Zalimuna,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu awo otchuka muwachite zomwe munachita Orebu ndi Zeebu ana a mafumu muwachite zomwe munachita Zeba ndi Zalimuna,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Muwaike akulu ao ngati Orebu ndi Zeebu; Mafumu ao ngati Zeba ndi Zalimuna: