Psalms 83:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Monga momwe moto umatenthera nkhalango, monga momwe malaŵi amayakira pa mapiri,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Monga moto upsereza nkhalango, ndi monga lawi liyatsa mapiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Monga moto umatentha nkhalango, kapena malawi a moto kuyatsa phiri,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Monga moto upsereza nkhalango, Ndi monga lawi liyatsa mapiri;