Psalms 83:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adziŵe kuti Inu nokha, amene dzina lanu ndinu Chauta, ndinu Wopambanazonse wolamulira dziko lonse lapansi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kuti adziwe kuti inu nokha, dzina lanu ndinu Yehova, ndinu Wam'mwambamwamba pa dziko lonse lapansi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Adziwe kuti Inu amene dzina lanu ndi Yehova, ndinu nokha Wammwambamwamba pa dziko lonse lapansi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kuti adziwe kuti inu nokha, dzina lanu ndinu Yehova, Ndinu Wam'mwambamwamba pa dziko lonse lapansi.