Psalms 83:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zoonadi, akumvana popangana chiwembu, akupangana zokuukirani,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti anakhalira upo ndi mtima umodzi; anachita chipangano cha pa Inu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndi mtima umodzi akukonzekera chiwembu; Iwo achita mgwirizano kutsutsana nanu:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti anakhalira upo ndi mtima umodzi; Anacita cipangano ca pa Inu: