Psalms 83:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Aasiriya nawonso agwirizana nawo, kuti alimbikitse mphamvu za ana a Loti.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Asiriya anaphatikana nao; anakhala dzanja la ana a Loti.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngakhalenso Aasiriya aphatikizana nawo kupereka mphamvu kwa ana a Loti. Sela
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Asuri anaphatikana nao; Anakhala dzanja la ana a Loti,