Psalms 83:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Muŵachite zomwe mudaŵachita Amidiyani, Sisera ndi Yabini ku mtsinje wa Kisoni,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Muwachitire monga munachitira Midiyani; ndi Sisera, ndi Yabini kumtsinje wa Kisoni,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Muwachitire zomwe munachitira Amidiyani, monga munachitira Sisera ndi Yabini ku mtsinje wa Kisoni.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Muwacitire monga munacitira Midyani; Ndi Sisera, ndi Jabini ku mtsinje wa Kisoni: